An Entrepreneur, Pro. Dj at Maximum Entertainment, Producer and Presenter of Friday Night Jamz on PL FM. Works at Chidren of the Nations Malawi

Joined June 2020
26 Photos and videos
A year older.
3
Classic
5
Maximum Events Garden. Opening Soon
11
Beautiful
15
A year older and wiser today. God is good
2
36
Pakati pa inuyo ndi bae amene amaponya zovala zakudza panja pa washing basket ndani?
Mbambande
Maximum Ghetto Festival 2021
Maximum Ghetto Festival 2021🔥
Kodi bwanji ma video a ma ukwati akunja sitiona ma photographer onyamula chi ambullera chija? 🙆‍♂️🤷‍♂️ asking for myself
Ndimati ndipempheko, Zija zomaima pa umba wa maliro "nkumati anawa tisamala ife achibale" bwanji zitasiika?
1
Mukasiyana lero ndikukumanaso mawa yamikani mulungu.
1
Anthu ena amazifila ngati opanda iwowo iweyo sungakhale.
On the move
1
Ma champagne poppers polani moto... zithuzi nzoti anthu amwe osati kuthila ma camera a anzanu..
1
Mmalo momuikiza mmapemphero mkazi chomuikira pa billboard ndi chani?
Mention your resident Pastor/Bishop/Prophet/Prophetes/overseer's name here or someone who impacted your life spiritually... let's show them some love..
Iwe ndalama ngati nchibisalilano chabwino wawina basi vumbuluka🤣
Guys you are now diluting the Amapiano genre and its fast losing salt. Leave the old school alone. You can't be doing remakes of all old time hits. Sizikukoma
Mwasowatu ngati wa police wa ndevu.